Ndikupereka

Ndikupereka
Performed by-
CategoryOffertory/Sadaka
Views3,406

Ndikupereka Lyrics

  1. Ndilibe mphotso ine zopereka kwa Mulungu wanga
    Ndiperekaine? Ndipereka moyo wanga *2

    Ndipereka ine?
    Ndipereka moyo wanga? *4

  2. Ndilibe chuma ine chopereka kwa Mulungu wanga
    Ndiperekaine? Ndipereka moyo wanga *2
  3. Ndilibe mwana ine wopereka kwa Mulungu wanga
    Ndiperekaine? Ndipereka moyo wanga *2